Lazarus Tembo lyrics

Nyimbo ya podyetsa mwana

Pa Monday ndi mpatsa mwana wanga, mukaka wa ufa
Mukaka wa ufa ndi wa bwino ku phala (lace la mwana wanga)
Paciwili ndi ma mpatsa, nshaba zo gaya
Nshaba zo sinja zimakoma ku phala (zipatsa mphamvu mwana wanga)
Pacitatu ndi ma mpatsa, kaela wo gaya
Kaela wo gaya ku phala a peleka mphavu

Chorus

Ndili ndi mwana wa mung’ono akula ndi mphavu
Ku phala lace ndiikako cakudya ca mphavu (uh!)
Ndicita ici pa masiku asanu ndi a wili
Kukwanitsa sabata limodzi kumwana wanga Pa cinai ndi ma mpatsa kapenta osinja

Kapenta ogaya amakoma ku phala (napatsa mphamvu mwana wanga)
Pa cisanu ndi ma mpatsa nsomba zo phika
Ndikaduladula bwino ndi ika ku phala (lace la mwana wanga)
Pa ciwelu ndi ma mpatsa, nyama yo phika
Nyama yo phika imakoma ku phala
Pa sabata ndi mpatsa dzila limodzi
Dzila lo phika limakoma ku phala

Chorus

Yimbaninso

ChorusOn Monday I give my child powdered milk
Powdered milk is good in porridge (of my child)
On Tuesday I give it pounded groundnuts
Pounded groundnuts is good in porridge (they make my child strong)
On Wednesday I give it ground beans
Ground beans in porridge gives strength

Chorus

I have got a small child, it is growing with strength
In its porridge I add strength giving foods (uh!)
I do this for seven days
Making one week for my child On Thursday I give it ground kapenta

Ground kapenta is good in porridge (and gives strength to my child)
On Friday I give it cooked fish
After chopping it I put it to the porridge (of my child)
On Saturday I give it cooked meat
Cooked meat is good in porridge
On Sunday I give it one egg
A boiled egg is good in porridge

Chorus

Sing again

ChorusTiyende Pamodzi Ndi UNIP

Sankani ndi kukumbukila, Nchito UNIP ya gwila mu Zambia
Kucokela pa tsiku la ufulu, Kufikila tsopano
Sankani ndi kukumbukila, A President Kenneth Kaunda
Ndi u sogoleli wao wa bwino, endani pa tsogolo ndi UNIP.

Ma primary schools ndi ma secondary schools (UNIP, Yes!)
Vipatala va tsopano mu Zambia yonse (UNIP, Yes!)
University ya Zambia ndi International Airport (UNIP, Yes!)
Mutendele mu dziko ndi kukhala bwino (UNIP, Yes!)
Miseo ya bwino mu Zambia yonse (UNIP, Yes!)
Kafue Hydro Scheme ndi Kafue textiles (UNIP, Yes!)

Kumbukilani nthawi izabwela, kusanka a imilili a UNIP
Mu ma Local Government elections, pitani pa tsogolo ndi UNIP
Tsopano tili ndi oil pipeline, Nakambala Sugar Estates
Ndi Ndola Copper Refinery, zonse izi ndi UNIP

Zambia Railways Sitima Sitima ya tsopano (UNIP, Yes!)
Mamangidwe a tsopano ndi nchito kwa onse (UNIP, Yes!)
Zambia Railways Sitima Sitima ya tsopano (UNIP, Yes!)
Mamangidwe a tsopano ndi nchito kwa onse (UNIP, Yes!)

Go With UNIP

Vote and remember what UNIP has done for Zambia
From the date of independence up to the present day
Vote and remember President Kenneth Kaunda
With his true leadership, You are going ahead with UNIP

More primary Schools, more secondary schools (UNIP, Yes!)
New hospitals throughout the country (UNIP, Yes!)
University of Zambia, International Airport (UNIP, Yes!)
Peace, progress, stability (UNIP, Yes!)
Good roads throughout the country (UNIP, Yes!)
Kafue hydro scheme and Kafue textiles (UNIP, Yes!)

So remember when the time comes to vote for UNIP chances
In the Local Government elections, so go ahead with UNIP
Now we have the oil pipeline, Nakambala Sugar Estates
Ndola Copper Refinery, all bacause of UNIP

Zambia Railways new diesel train (UNIP, Yes!)
Local industries, more jobs for all (UNIP, Yes!)
Zambia Railways new diesel train (UNIP, Yes!)
Local industries, more jobs for all (UNIP, Yes!)

Many thanks to Edwin Nyirenda for the lyrics!